Lyrics Sindichoka (feat. Beracah) - Gwamba
Zambiri
yanu
ndinamva
akhungu
onse
osamva
enawo
sayenda
kungowakhuza
Inu
nyengo
zawo
zinasitha
nane
ndifuna
mundikhudze
chonde
Musandipitilire
ndatsegula
manja
mulore
zimu
wanu
mwa
ine
ukhazikike
Yesu
anamva
mphamvu
zikuchoka
zimai
wina
wina
wake
atugwira
mavuto
Ake
onse
ndikuchoka
amadwala
bas
iye
ndi
kuchira
nane
mbuye
wanga
Mundigunde
mukandiolose
pa
mafunde
ndikudziwa
pena
Ndine
khutukumve
koma
mukafuna
kukandi
user
mundi
user
Mukandikhudza
nyengo
zanga
zisitha
mukandikhuza
nyengo
zanga
Mumachita
zazikulu
izo
ndinamva
simkaika
konse
I
wanna
see
your
glory
I
wanna
testify
ukulu
wanu
ndiuone
kma
sindichokachokachoka
mpaka
Mundikhudzekhudzekhudze
kma
Sindichokachokachoka
mpaka
mundikhudze
ine
Mbuye
wanga
chonde
mundikhudze
ndikalakwisa
chonde
mundiuze
Ndikamachepa
chonde
mundikuuze
osalora
satana
andi
zunze
zolakwika
Zonse
muzichotse
inu
ndamene
mungakonze
pandekhapa
palibe
Chomwe
ndingachite
nde
chonde
muzindisamalira
nthawi
zonse
Chonde
musalore
moyo
wanga
satana
adzaleponso
adzalemo
zoti
Sizanga
chonde
musalore
mbuye
wanga
satana
akolope
moyo
mwanga
Mukandikhudza
nyengo
zanga
zisitha
mukandikhudza
nyengo
zanga
Mumachita
zazikulu
izo
ndinamva
simkaika
konse
I
wanna
see
your
glory
I
wanna
testify
ukulu
wanu
ndiuone
kma
Sindichokachokachoka
mpaka
mundikhudzekhudzekhudze
Kma
sindichokachokachoka
mpaka
mundikhudze
khudze
ine
Mpaka
mundikhuze
ine
END
1 Oba (feat. Nimix & Tay Grin)
2 You Are Everything (feat. Tumi)
3 Mtima Pansi (feat. Onesimus)
4 Final Say (feat. Dan Lu)
5 Akondakitale (feat. Lawi)
6 Sindichoka (feat. Beracah)
7 48 Bars for Christ
8 Unatha
9 That's a No No (feat. Jillz)
10 Higher (feat. Nimix)
11 Give Me Love (feat. Praise Peterson)
Attention! Feel free to leave feedback.