Eli Njuchi - Ziloleni текст песни

Текст песни Ziloleni - Eli Njuchi



Mamawa dzuwa kuli mame
You see me passing by everyday
M'manja muli saka
I know you follow me
Muma ndi londola mobisa
Pomwe ndadusa pamakhala mbeu
Mukandifunsa sin'bisa
Ndine mlimi
Kwanga nkufesa
Mbeu yangayi njowala
Ngati nyenyezi
Ndikawawuza nde samandimvesa
Chita manyazi
Ziloleni
Ziphukile
Ziloleni
Ziphukile
Ndati lolani ziphukile ngati mtengo
Ngati nthambi zibale zipatso
Ziloleni
Ziphukile
Ziloleni
Ziphukile
Ziloleni
Ziphukile
Lolani ziphukile ngati mtengo
Ngati nthambi zibale zipatso
Ziloleni
Ziphukile
Ok sispensa
Tiye tiyambilenso
Mamawa mpaka kumadzulo
Ntchito
Yako malipiro
Siwu zina zimapondedwa
Zina kudyedwa ndi mbalame
Zochepa zingapo zimasamalidwa
Zimandikhudza nsaname
Mbeu zipase musaziyang'anire
Ndiza ntsogolo zizandisamalire
Ndipo musadabwe nkati ndi thilire
Zimela zagwerapo olo mundisesele
Olo musazitipulire
Muzazi wona zikukula
Olo musazitipulire
Muzazi wona muzazi wona zikukula
Ziloleni
Ziphukile
Ziloleni
Ziphikile
Ndati lolani ziphukile ngati mtengo
Ngati nthambi zibale zipatso
Ziloleni
Ziphukile
Ziloleni
Ziphukile
Ziloleni
Ziphukile (ooh)
Lolani ziphukile ngati mtengo
Ngati nthambi zibale zipaso
Ziloleni
Ziphukile
Zili ngati mwini nyimbo
Lolani ndifese mbeu yaluso
Musandiweluze kamba ka nsinkhu
(Ooh yeah)
Abale fesani mbeu
Ziphukile
Musazibise fesani
Ziphukile



Авторы: Eli Njuchi


Eli Njuchi - The Book of Eli
Альбом The Book of Eli
дата релиза
16-12-2020




Внимание! Не стесняйтесь оставлять отзывы.